by Gift Tembo
July 12th 2026.
#WCMzamasewero

Timu ya Silver Strikers yatuluka muchikho cha Airtel Top8 itagonja ndi timu ya Karoga United ndi zigoli zitatu kwa duu pabwalo la Karonga. 

Silver Strikers imalowa mmasewerowa ikutsogola ndi zigoli ziwiri kwa duu zomwe anagoletsa pabwalo la Silver mgawo loyamba lamasewero a mpikisanowu, zomwe zikutanthauza kuti pamasewero awiri Silver Strikers yagonja ndi zigoli zitatu kwa ziwiri(3-2).

Mmasewero ena timu ya Mighty wanderers yafikaso mndime yamatimu anayi italepherana ndi Creck Sporting pogoletsana chigoli chimodzi kwa chimodzi koma pamasewero oyamba timuyi inapambana ndi zigoli ziwiri kwa duu, pamasewero awiri yapambana (3-1).

Zateremu mu ndime yamatimu anayi Mighty Wanderers izakumana ndi Karonga United pomwe Blue Eagles izasosolana nthenga ndi Ekhaya FC. 

Wolemba:Noel Mtanga-Lilongwe(12/7/2026).
Search Website

Search

Explore

Categories

Explore

Tags

Subscribe

Newsletter

Explore

Similar websites

WhatsApp Google Map

Safety and Abuse Reporting

Thanks for being awesome!

We appreciate you contacting us. Our support will get back in touch with you soon!

Have a great day!

Are you sure you want to report abuse against this website?

Please note that your query will be processed only if we find it relevant. Rest all requests will be ignored. If you need help with the website, please login to your dashboard and connect to support